Let's do ndi mndandanda wa maphunziro ya aphunzi ocokera mu Giredi 1 kufikira mu Giredi 7 ndi ndondomeko zoyenera kutsatira pokwaniritsa ndodomeko ya mitu ya maphunziro yonse. Yolembedwa ndi akatswiri pa gulu la aphunzi awa, zocita zimatangwanitsa aphunzi mu njira za maphunziro awo a zocita ndi manja ndi kuikako nzeru ku maphunziro kupyolera mu zocita-cita.