Let's do ndi mndandanda wa maphunziro ya aphunzi ocokera mu Giredi 1 kufikira mu Giredi 7 ndi ndondomeko zoyenera kutsatira pokwaniritsa ndodomeko ya mitu ya maphunziro yonse. Yolembedwa ndi akatswiri pa gulu la aphunzi awa, zocita zimatangwanitsa aphunzi mu njira za maphunziro awo a zocita ndi manja ndi kuikako nzeru ku maphunziro kupyolera mu zocita-cita

Let's do musango wamabuuku uubiika abasambi pakati ka masambililo yabo ukufuma mu Geledi 1 ukufika namu Geledi 7. Muntampulo shonse, kulaba ukukonka ubutantiko na ukumona ukuti fyonse ifyatantikwa mu silabasi fya fundwa. Incenshi shalemba shalimona ukuti imilimo yabasambi mufitabo ifwaikwa ukucitilwa mumusango uo abasambi bengasambilila ukupitila mukuibombela abene.